Ask AI
ProCE Banner Activity

Thanzi la Amayi Ndi Thanzi la Dera Lonse: Kuphatikiza PrEP mu Zithandizo za ku Dera Kuti Tithetse HIV

Clinical Thought

Ku Sub-Sahara Africa, mliri wa HIV sumakhudza anthu okha, koma madera onse. Pitirizani kuwerenga kuti mudziwe chifukwa chomwe kuphatikizira chisamaliro cha omwe ali ndi kachilombo ka HIV komanso kupewa kachirombo ka HIV ndi zithandizo za ku dera kuli kofunika kwambiri popewa kufala kwa kachilombo komanso momwe zingathandizire kuposa munthu  payekha.

Released: March 02, 2026

Share

Provided by

Provided by Clinical Care Options, LLC dba Decera Clinical Education in partnership with the Foundation for Professional Development

ProCE Banner

Supporters

Supported by an educational grant from Gilead Sciences, Inc.

Gilead Sciences, Inc.

Partners

Foundation for Professional Development

ProCE Banner

Target Audience

This activity is intended for doctors, nurses, and allied healthcare workers who provide care in sub-Saharan Africa.

Learning Objectives

Upon completion of this activity, participants should be able to:

  • Phatikizani maphunziro othandiza kuchokera ku mapulogalamu omwe adatheka a PrEP mu chisamaliro chawo cha odwala kuti awonetsetse kuti ntchito za PrEP ndizolunjika pa anthu, zopanda kusalana, zosavuta kupeza, zogwirizana ndi zithandizo zina, komanso zokhazikika.

Disclosure

Primary Author

Nelly Rwamba Mugo, MBChB, MMed, MPH: consultant/advisor/speaker: MSD.